
A Malawi alire bwanji? Sugar wakwelanso
Advertisement Pomwe aMalawi ambiri akudandaula ndi kukwera kwa katundu osayinasiyana m’dziko muno, kampani ya Illovo Sugar yakwezanso mtengo wa sugar. Malinga ndi kampaniyi paketi ya sugar ya 1kg tsopano izigulitsidwa pa mtengo wa K3000. Kampaniyi yati …